Mawu a M'munsi Mawu akuti “ana a aneneri” mwina akutanthauza sukulu yopereka malangizo kwa aneneri, kapena bungwe la aneneri.