Mawu a M'munsi Zikuoneka kuti wamasomphenya anali munthu amene Mulungu ankamuchititsa kuti azitha kudziwa chifuniro cha Mulunguyo.