Mawu a M'munsi “Mule” ndi madzi onunkhira ochokera kumitengo inayake, ndipo nthawi zina madziwa anali kupangira mafuta odzola.