Mawu a M'munsi
Pa nthawi ya Mfumu Davide, Aisiraeli anali ndi maulonda a usiku atatu. Ulonda woyamba unkayamba 6 koloko madzulo mpaka 10 koloko usiku. Ulonda wachiwiri unkayamba 10 koloko usiku mpaka 2 koloko usiku, ndipo ulonda wachitatu unkayamba 2 koloko usiku mpaka 6 koloko m’mawa.