Mawu a M'munsi “Mankhusu” ndi makoko amene amachotsa kumbewu ngati mpunga popuntha, ndipo amatha kuwauluza ndi mphepo.