Mawu a M'munsi “Petulo” amatchedwa ndi mayina asanu. Pano akutchedwa “Simoni, wotchedwa Petulo.” Pa Mt 16:16 akutchedwa “Simoni Petulo,” pa Mac 15:14, “Sumeoni,” ndipo pa Yoh 1:42, “Kefa.” Koma nthawi zambiri amatchedwa “Petulo,” monga mmene zilili pa Mt 14:28.