Mawu a M'munsi Kutanthauza chovala chimene nsalu yake anaiwomba mophatikiza ulusi wathonje ndi ubweya wankhosa. Onani De 22:11.