Mawu a M'munsi Nʼkutheka kuti dzina lakuti Yabezi linachokera ku mawu a Chiheberi omwe amatanthauza “ululu.”