Mawu a M'munsi “Petulo” amadziwika ndi mayina 5. Pano akutchulidwa kuti “Simoni, amene ankatchulidwa kuti Petulo.” Pa Mt 16:16 akutchulidwa kuti “Simoni Petulo,” pa Mac 15:14, “Sumiyoni,” ndipo pa Yoh 1:42, “Kefa.” Koma nthawi zambiri amatchulidwa kuti “Petulo,” monga mmene zilili pa Mt 14:28.