Mawu a M'munsi
a Nkhaniyi sikulozera ku mkhalidwe wosakhoza kupiririka kotheratu mu umene wachichepere wawunikiridwa ku kuipsyidwa kwa kuthupi kapena kwa kugonana. M’nkhani zoterozo, wachichepere angafunikire kufunafuna thandizo lochokera kwa akatswiri kunja kwa banja. Onani “Kugonana kwa Pachibale—Upandu Wobisika” m’kope lathu la February 8, 1981, Chingelezi.