Mawu a M'munsi a Mbale wa Abramu Nahori anatsala kumbuyo, mwinamwake kuti amalize kusamalira malonda ake kapena zinthu zina zaumwini. Koma pambuyo pake mbadwa za Nahori zinachokanso ku Uri ndi kulambira Yehova mu Harana.—Genesis 11:31; 24:1-4, 10, 31; 27:43; 29:4.