Mawu a M'munsi
b Kawonedwe kofala kakuti Chisilamu chiri kwenikweni chipembedzo cha Chiarabu kali kolakwika. Unyinji wa Asilamu amakono sali Aarabu. Indonesia, dziko lokhala ndi Asilamu ochuluka koposa, liri ndi omamatira ku chipembedzocho 150Â miliyoni.