Mawu a M'munsi
a Mu phunziro lina, 25 peresenti ya ophunzira m’makalasi oyambirira a ku sukulu yapamwamba a mu U.S. anandandalitsa “ovutitsa ndi mkhalidwe wosokoneza” monga chodetsa nkhaŵa chachikulu. Mu Great Britain ndi West Germany, ophunzitsa mofananamo alongosola kudera nkhaŵa kuti kuvutitsa kwawonjezeka m’kuchitika ndi kuipa.