Mawu a M'munsi
b Kaamba ka zochititsa kulekana kwa muukwati, onani nkhani yakuti “Nchifukwa Ninji Amayi ndi Atate Analekana?” m’kope la April 8, 1988, la Galamukani! Onaninso nkhani za “Achichepere Akufunsa Kuti . . . ” m’makope a December 22, 1987, (Chingelezi) ndi July 8, 1988.