Mawu a M'munsi
b Chiyambire zaka za zana loyamba B.C.E., nyumba za Ayuda zakhala zikusonyeza kandulo loyatsidwa imodzi patsiku loyamba la madyererowo, makundulo aŵiri oyatsidwa patsiku lachiŵiri, ndikunkabe tero masiku asanu ndi atatu onsewo. Kachitidweka kadakakumbukiridwabe ndi Ayuda lerolino.