Mawu a M'munsi
c Minkhole yambiri imachitidwa choipa ndi atate awo enieni kapena atate opeza. Ochitira zoipa angakhalenso akulu awo, amalume, agogo aamuna, odziƔana nawo achikulire, ndi alendo. Popeza kuti minkhole yambiri ndi akazi, kwakukulukulu tidzalozera kwa iwo. Komabe, chidziƔitso choperekedwa pano chimagwira ntchito kwa onse.