Mawu a M'munsi
a Liwu lomasuliridwa ‘kubwerezabwereza’ (bat·ta·lo·geʹo) lagwiritsiridwa ntchito kamodzi kokha m’Baibulo ndipo limatanthauza “‘kubwebweta’ mwakuyesa kupeza chipambano m’pemphero mwakuchulukitsa mawu amodzimodzi.”—Theological Dictionary of the New Testament.