Mawu a M'munsi
a Panthaŵi zina kuikidwa m’chisamaliro cha magulu oyang’anira okalamba nkofunika. Komabe ngakhale zitatero, ana ayenera kuchezera makolo awo nthaŵi zonse ndi kuwathandiza monga momwe angathere. Wonani Nsanja ya Olonda ya June 1, 1987.