Mawu a M'munsi
c “Cholinga cha chiwawacho sindicho mchitidwe wa ‘kugonana’ koma mmalo mwake mchitidwe wa kugonanawo ndiwo chida chimene waliwongoyo amagwiritsira ntchito kuchita upandu wa chiwawa.”—Wanda Keyes-Robinson, mkulu wa chigawo cha, Sexual Offense Unit, Baltimore City, Maryland.