Mawu a M'munsi
a Palibe mikhalidwe iƔiri imene iri yofanana, ndipo palibe uphungu wa kupewa umene uli wogwira mtima koposa. Ngakhale akatswiri pankhani za kugwirira chigololo samavomerezana ponena za mlingo ndi mtundu wa kukaniza zimene mkhole uyenera kupanga pakuukiridwako.