Mawu a M'munsi
a Mkhole wamasuliridwa kukhala “munthu amene amavulazidwa kapena kuphedwa ndi wina . . . Amene amavulazidwa kapena kuvutitsidwa ndi chochitika, ngozi, nthumwi, kapena mkhalidwe.” Kumbali ina, wophedwera chikhulupiriro ali “amene amasankha kufa m’malo mokana zikhulupiriro zachipembedzo. . . . Amene amadzimana kwakukulu kapena kuvutika kwambiri kotero kuti achilikize chikhulupiriro, cholinga, kapena lamulo lamkhalidwe.”—The American Heritage Dictionary of the English Language, Kope Lachitatu.