Mawu a M'munsi
a Chiphunzitso china chotero ndicho lingaliro la Aprotesitanti osunga mwambo lakuti “mlungu” wa kulenga wotchulidwa m’Genesis ndiwo sabata la masiku enieni a maola 24. Baibulo limasonyeza kuti iwo kwenikweni anali nyengo ya zaka zikwi zambirimbiri.