Mawu a M'munsi
b Kusudzula kuti muchoke kwa mnzanu wamuukwati wachigololo kuli chosankha chaumwini. Kuti muone mafotokozedwe a mfundo zosiyanasiyana zimene wamuukwati wosalakwa ayenera kuzipenda posankha kuti kaya ayenera kupeza chisudzulo cha Malemba, chonde onani makope a Nsanja ya Olonda a August 15, 1993, tsamba 5, ndi May 15, 1988, masamba 4 mpaka 7.