Mawu a M'munsi
b Ngati mwachita tondovi kapena mukulimbana ndi zisonkhezero za kudziwononga, bwanji osalankhula ndi winawake ndi kupeza thandizo mmalo modziika pa maupandu osayenerera?—Onani “Achichepere Akufunsa Kuti . . . Kodi Kudzipha Ndiko Yankho?” m’kope lathu la Galamukani! la April 8, 1994.