Mawu a M'munsi
a “Akatswiri ena amakhulupirira kuti mumakhala wonenepetsa ngati muposa ndi 20 peresenti kulemera ‘koyenera’ . . . kolingana ndi kutalika kwanu, kaumbidwe ka thupi ndi usinkhu.”—The American Medical Association Family Medical Guide, tsamba 501. Onaninso Galamukani! wa May 8, 1994, “Achichepere Akufunsa Kuti . . . “Kodi Ndingachepetse Motani Thupi?” ndi June 8, 1989, “Kodi Kutaya Kulemera Kuli Nkhondo Yosagonjetseka?”