Mawu a M'munsi
b Zitsanzo zina za matenda opatsirana mwa kugonana: Padziko lonse pali anthu pafupifupi 236 miliyoni odwala trichomoniasis ndipo anthu pafupifupi 162 miliyoni ali ndi matenda a chlamydia. Chaka chilichonse pamakhala anthu pafupifupi 32 miliyoni amene amadwala njereĊµere zakumpheto, 78 miliyoni chinzonono, 21 miliyoni matuza akumpheto, 19 miliyoni chindoko, ndi 9 miliyoni chancroid.