Mawu a M'munsi
a Ruth Danner anatumizidwa kwina pa usinkhu wa zaka zisanu ndi zinayi limodzi ndi makolo ake ndipo anamangidwa m’misasa isanu ndi umodzi yosiyanasiyana. Onani 1980 Yearbook of Jehovah’s Witnesses, yofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc., tsamba 105.