Mawu a M'munsi
a Ngati mufuna mafotokozedwe atsatanetsatane a chimene Ufumu wa Mulungu uli ndi mmene udzapindulitsira anthu okhulupirira, chonde Ɣerengani buku la ChidziƔitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.