Mawu a M'munsi
a Matenda ena a nkhaŵa ndi monga kupanikizika maganizo, obsessive-compulsive disorder, kuopa masoka akale, ndi matenda ena a nkhaŵa. Kuti mumve zambiri, onani Galamukani! yachingelezi ya February 8, 1996, “Compulsive Behavior—Does It Control Your Life?” ndi June 8, 1996, “Coping With Panic Attacks.”