Mawu a M'munsi
a Zimenezi sizinachititse kuti akazi asanduke anthu otsikirapo m’mabanja, kuti iwo ndi oyenera ntchito za m’nyumba kapena za kumunda basi. Zimene Baibulo limafotokoza za “mkazi wangwiro” m’buku la Miyambo zimaonetsa kuti mkazi wokwatiwa sankangosamalira banja lokha komanso ankasamalira zinthu zambiri za pakhomo, ankalima n’kumapeza chakudya chokwanira, ndiponso kugulitsa malonda.— Miyambo 31:10, 16, 18, 24.