Mawu a M'munsi
a Mungathe kudziŵa chiwongola dzanja chimene kampani inayake ya makadi a ngongole imalipiritsa poyang’ana mbali yotchedwa annual percentage rate (APR) imene imalembedwa pa kalata yofunsira kapena pa kalata yokumbutsa ngongole yapamwezi.