Mawu a M'munsi
c Mabungwe asanu ndi limodzi ameneĊµa ndiwo bungwe la UNICEF, la United Nations Development Programme, la United Nations Population Fund, la World Health Organization, la World Bank, ndi la United Nations Educational, Scientific, and Cultural Organization. Bungwe la UNAIDS analikhazikitsa mu 1995.