Mawu a M'munsi
b Magulu a nyenyezi 48 ameneŵa anali kudziŵika ku Mesopotamiya, ku Mediterranean ndiponso ku Ulaya. Kenaka, maguluŵa anadziŵikanso kwa anthu amene anasamukira ku Kumpoto kwa America ndi ku Australia. Komabe, anthu ena, monga ngati Atchaina ndi Aindiya a ku Kumpoto kwa America anagaŵa thambo mosiyana.