Mawu a M'munsi
b Malingana ndi zimene ananena wofufuza wotchedwa Sara McLanahan ndi Gary Sandefur, ku United States, “pafupifupi ana 40 mwa ana 100 aliwonse amene amati n’ngoyenera kulandira chithandizo alibe lamulo [loperekedwa kukhoti] lakuti anawo athandizidwe, ndipo mmodzi mwa anayi alionse amene ali ndi lamuloli salandira chilichonse. Ana amene amalandira zonse zowayenerera ndi mmodzi mwa atatu alionse.”