Mawu a M'munsi
d Buku lotchedwa Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja (Lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.) lili ndi malangizo ambiri ochokera m’Baibulo amene angathandize mabanja. Mungalipeze popezana ndi a Mboni za Yehova kwanuko.