Mawu a M'munsi
a Mosiyana ndi zimenezi, La Niña (mawu a chilankhulo cha Chisipanya otanthauza kuti “kamtsikana”) n’kuzizira kwa madzi pa nyengo zinazake m’dera la gombe lakumadzulo kwa South America. La Niña nayenso amakhudza zochitika zanyengo m’madera akutali.