Mawu a M'munsi
b Zizindikiro za nthenda ya HD ndiponso kufulumira kuonekera kwake zingakhale zosiyana kwambiri pakati pa anthu osiyanasiyana. Choncho, zizindikiro zimene talongosola panozi zaperekedwa kuti zikupatseni chithunzithunzi chabe ndipo sikuti zakonzedwa mwatsatanetsatane kotero kuti n’kuzigwiritsira ntchito pofuna kupeza nthendayi ayi.