Mawu a M'munsi
c Zaka zimene munthu wodwala HD amayembekezeka kukhalabe ndi moyo ndi pafupifupi 15 mpaka 20 kuchokera pamene zizindikiro za nthendayi zayamba, ngakhale kuti ena amakhala ndi moyo kwakanthaŵi ndithu. Nthaŵi zambiri wodwalayo amafa chifukwa cha chibayo popeza kuti satsokomola mokwanira kuti achotse makhololo amatenda m’chifuwa.