Mawu a M'munsi
a Tagwiritsa ntchito dzina lakuti “multiple chemical sensitivity” chifukwa chakuti ndilo dzina lotchuka kwambiri. Koma palinso mayina ena ambiri, monga “environmental illness” ndi “chemical hypersensitivity syndrome.” Mawu onseŵa akutanthauza kuti anthu ena amakhudzidwa ndi mankhwala ngakhale mankhwalawo atakhala pamlingo woyenerera kwa anthu ambiri.