Mawu a M'munsi
a Ngati kuvutika maganizo kukupitirizabe, kungasonyeze matenda aakulu athupi kapena amaganizo. Motero, ndi bwino kupita kuchipatala msanga. Onani nkhani yakuti “Kupambana Nkhondo Yolimbana ndi Kuchita Tondovi” m’kope la March 1, 1990 la magazini inzake ya magazini ano yotchedwa Nsanja ya Olonda.