Mawu a M'munsi
a Kutopa kwa nthaŵi yaitali kungayambe kapena kukula ndi zinthu zingapo kuwonjezanso zopsinja za tsiku ndi tsiku. Kungayambe chifukwa chodwala, zakudya zopereŵera, mankhwala osokoneza bongo, kuipitsa dziko ndi makemikolo, kuvutika maganizo ndi mtima, ukalamba, kapena chifukwa cha zonse zimenezi.