Mawu a M'munsi
a Zimene Schlabach ananena n’zogwirizana ndi zimene Danieli analosera kuti Ufumu wa Roma ukagonjetsedwa ndi mphukira yake. Onani mitu 4 ndi 9 ya buku la Samalani Ulosi wa Danieli!, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.