Mawu a M'munsi
a Mayiko 15 odzilamulira okha amene anali mumgwirizano wa Soviet Union ndi awa: Armenia, Azerbaijan, Belarus, Estonia, Georgia, Kazakhstan, Kyrgyzstan, Latvia, Lithuania, Moldova, Russia, Tajikistan, Turkmenistan, Ukraine, ndi Uzbekistan.