Mawu a M'munsi
a Dziko lapansi linagaŵidwa m’zigawo za maluŵa zisanu n’chimodzi. Akatswiri oona madera amene zomera zimapezeka anagaŵa zigawozi malingana ndi zomera zimene zimapezekako. Dera lozungulira chigawo cha Cape ku South Africa lili m’gulu la zigawo zisanu ndi chimodzi zimenezi.