Mawu a M'munsi
a Buku lakuti Phunzirani Kuŵerenga ndi Kulemba (lomwe lili m’zinenero 6) ndiponso buku lina latsopano kwambiri lakuti Dziperekeni pa Kuŵerenga ndi Kulemba (lomwe lili m’zinenero 29) n’ngofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Funsani ku Nyumba ya Ufumu yakwanuko kapena olemba magazini ino kuti mupeze buku lanulanu kwaulere.