Mawu a M'munsi
a Anthu ena amaganiza kuti ngakhale kuti ambiri amabadwa nalo vutoli, palinso ena amene amabadwa ali abwinobwino ndipo kenaka akakumana ndi zoopsa zina ubongo wawo umasokonezeka motero angathe kuvutika maganizo mosavuta.