Mawu a M'munsi
a Akuti matenda ena, monga kuchuluka kwa madzi a m’magazi, matenda ochuluka kwambiri shuga, kupereŵera magazi, matenda a chithokomiro ndiponso kupereŵera kwambiri kwa shuga m’thupi, zizindikiro zake zimafanana ndi za munthu wovutika maganizo.