Mawu a M'munsi
b N’chimodzimodzinso masiku ano, Akristu ena amalemba anzawo ntchito; ena amalembedwa ntchito. Mongadi mmene Mkristu wolemba mnzake ntchito sangazunze anthu amene akum’gwirira ntchito, ophunzira a Yesu m’zaka za zana loyamba akanachitiranso akapolo mogwirizana ndi mfundo za Chikristu.—Mateyu 7:12.