Mawu a M'munsi
c Kuti mudziŵe zambiri za chiphunzitso cha Baibulo pankhani ya chiukiriro, onani mutu 9 wakuti “Kodi N’chiyani Chimachitika kwa Okondedwa Athu Akufa?” womwe uli m’buku la Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.