Mawu a M'munsi
a Ena mwa matendaŵa ndiwo nyamakazi yochokera m’madzi a mfundo za mafupa, nyamakazi imene imadya mafupa pamfundo, ya pakhungu, yokonda kugwira ana ndiponso achinyamata, ya m’mapewa kapenanso akasukusuku, ya pakhungu yofalitsidwa ndi nthata, yofoola manja, ya m’minyewa, ya m’maso, ndiponso ya msana.